Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 98:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  4 Fuulirani Yehova mosangalala chifukwa wapambana, inu nonse anthu a padziko lapansi.+

      Kondwerani, fuulani mosangalala ndi kuimba nyimbo zomutamanda.+

  • Yesaya 41:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Ndakutenga kuchokera kumalekezero a dziko lapansi,+ ndiponso ndakuitana kuchokera kumadera akutali a dziko lapansi.+ Chotero ndinakuuza kuti, ‘Iwe ndiwe mtumiki wanga.+ Ndasankha iweyo+ ndipo sindinakutaye.+

  • Yesaya 42:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Imbirani Yehova nyimbo yatsopano.+ M’tamandeni kuchokera kumalekezero a dziko lapansi.+ M’tamandeni inu amuna amene mumadalira nyanja+ ndi zonse zokhala mmenemo, ndiponso inu zilumba ndi anthu okhala m’zilumbazo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena