Ekisodo 8:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pamenepo Farao anayankha kuti: “Mawa.” Ndiyeno Mose anati: “Zidzachitika monga mwa mawu anu, kuti mudziwe kuti palibenso wina wofanana ndi Yehova Mulungu wathu,+ Ekisodo 15:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndi mulungu wina uti amene angafanane nanu, inu Yehova?+Ndinu woyera kopambana, ndani angafanane ndi inu?+Ndinu woyenera kuopedwa+ ndi kukuimbirani nyimbo zotamanda.+ Inu ndinu wochita zodabwitsa.+ Salimo 113:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndani angafanane ndi Yehova Mulungu wathu,+Amene amakhala pamwamba?+ Yesaya 40:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 “Koma kodi anthu inu mungandiyerekezere ndi ndani kuti ndifanane naye?” akutero Woyerayo.+ Yeremiya 10:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndithudi palibe aliyense wofanana ndi inu Yehova.+ Inu ndinu wamkulu, ndipo dzina lanu ndi lalikulu ndi lamphamvu.+
10 Pamenepo Farao anayankha kuti: “Mawa.” Ndiyeno Mose anati: “Zidzachitika monga mwa mawu anu, kuti mudziwe kuti palibenso wina wofanana ndi Yehova Mulungu wathu,+
11 Ndi mulungu wina uti amene angafanane nanu, inu Yehova?+Ndinu woyera kopambana, ndani angafanane ndi inu?+Ndinu woyenera kuopedwa+ ndi kukuimbirani nyimbo zotamanda.+ Inu ndinu wochita zodabwitsa.+
6 Ndithudi palibe aliyense wofanana ndi inu Yehova.+ Inu ndinu wamkulu, ndipo dzina lanu ndi lalikulu ndi lamphamvu.+