Ekisodo 19:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Tsopano ngati mudzalabadiradi+ mawu anga ndi kusunga pangano langa,+ pamenepo mudzakhaladi chuma changa chapadera pakati pa anthu ena onse,+ chifukwa dziko lonse lapansi ndi langa.+ 2 Mafumu 1:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndiyeno mngelo+ wa Yehova anauza Eliya wa ku Tisibe+ kuti: “Nyamuka ukakumane ndi amithenga a mfumu ya ku Samariya, ndipo ukawafunse kuti, ‘Kodi ku Isiraeli kulibe Mulungu+ kuti mupite kukafunsa kwa Baala-zebubu mulungu wa ku Ekironi? Salimo 135:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ya wadzisankhira Yakobo,+Wadzisankhira Isiraeli kukhala chuma chake chapadera.+
5 Tsopano ngati mudzalabadiradi+ mawu anga ndi kusunga pangano langa,+ pamenepo mudzakhaladi chuma changa chapadera pakati pa anthu ena onse,+ chifukwa dziko lonse lapansi ndi langa.+
3 Ndiyeno mngelo+ wa Yehova anauza Eliya wa ku Tisibe+ kuti: “Nyamuka ukakumane ndi amithenga a mfumu ya ku Samariya, ndipo ukawafunse kuti, ‘Kodi ku Isiraeli kulibe Mulungu+ kuti mupite kukafunsa kwa Baala-zebubu mulungu wa ku Ekironi?