Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mafumu 25:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Iwo anapha ana a Zedekiya iye akuona,+ kenako Zedekiyayo anam’chititsa khungu.+ Atatero anamumanga ndi maunyolo amkuwa+ n’kupita naye ku Babulo.+

  • Yeremiya 21:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Anthu amene adzakhalabe mumzindawu adzafa ndi lupanga, njala yaikulu ndiponso mliri.+ Koma amene adzatuluka ndi kugwidwa ndi Akasidi amene akuzungulirani adzakhala ndi moyo. Iwo adzapulumutsa moyo wawo.”’+

  • Yeremiya 42:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 ndiye kuti lupanga limene mukuliopa lidzakupezani ku Iguputo+ komweko ndipo njala yaikulu imene mukuithawa idzakutsatirani ku Iguputoko+ moti mudzafera komweko.+

  • Ezekieli 26:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Anthu okhala m’midzi yozungulira imene ili kunja kwa mzindawu adzawapha ndi lupanga. Iwo adzakumangira mpanda womenyerapo nkhondo ndi chiunda chomenyerapo nkhondo,+ ndipo adzadziteteza ndi chishango chachikulu.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena