Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 34:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Yehova ali ndi lupanga. Lupangalo lidzakhala magazi okhaokha+ ndipo lidzaterera ndi mafuta. Lidzadzaza magazi a nkhosa zamphongo zing’onozing’ono ndi a mbuzi zamphongo. Lidzaterera ndi mafuta+ a impso za nkhosa zamphongo, pakuti Yehova adzapereka nsembe ku Bozira ndipo adzapha nyama zambiri m’dziko la Edomu.+

  • Yeremiya 50:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Iphani ng’ombe zake zonse zazing’ono zamphongo.+ Zonse zipite kokaphedwa.+ Tsoka kwa iwo, chifukwa tsiku lawo lafika. Nthawi yoti alangidwe yafika.+

  • Ezekieli 39:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Mudzadya mnofu wa anthu amphamvu,+ mudzamwa magazi a atsogoleri a dziko lapansi, nkhosa zamphongo, ana a nkhosa amphongo,+ mbuzi zamphongo ndi ng’ombe zamphongo.+ Zonsezi ndi nyama zonenepa za ku Basana.+

  • Zekariya 10:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 “Mkwiyo wanga wayakira abusa,+ ndipo atsogoleri awo oipa ngati mbuzi+ ndiwaimba mlandu.+ Pakuti ine Yehova wa makamu ndacheukira gulu langa la nkhosa.+ Ndacheukira nyumba ya Yuda ndipo ndaisandutsa hatchi+ yanga yaulemerero, yokwera popita kunkhondo.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena