2 Mafumu 24:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Mfumu ya Iguputo sinatulukenso+ m’dziko lake,+ chifukwa mfumu ya Babulo inali itatenga zinthu zonse zomwe zinali za mfumu ya Iguputo,+ kuyambira kuchigwa*+ cha Iguputo kukafika kumtsinje wa Firate.+ Yesaya 20:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Iwo adzachita mantha ndiponso manyazi chifukwa chakuti anali kudalira Itiyopiya+ komanso chifukwa chakuti anali kusirira kukongola kwa Iguputo.+ Maliro 1:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ndaitana anthu ondikonda kwambiri,+ koma anthuwo andichitira zachinyengo.Ansembe anga ndiponso akuluakulu atha+ mumzinda.Atha pamene anali kufunafuna chakudya choti adye kuti adzitsitsimutse.+
7 Mfumu ya Iguputo sinatulukenso+ m’dziko lake,+ chifukwa mfumu ya Babulo inali itatenga zinthu zonse zomwe zinali za mfumu ya Iguputo,+ kuyambira kuchigwa*+ cha Iguputo kukafika kumtsinje wa Firate.+
5 Iwo adzachita mantha ndiponso manyazi chifukwa chakuti anali kudalira Itiyopiya+ komanso chifukwa chakuti anali kusirira kukongola kwa Iguputo.+
19 Ndaitana anthu ondikonda kwambiri,+ koma anthuwo andichitira zachinyengo.Ansembe anga ndiponso akuluakulu atha+ mumzinda.Atha pamene anali kufunafuna chakudya choti adye kuti adzitsitsimutse.+