Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Miyambo 19:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Kupusa kwa munthu wochokera kufumbi n’kumene kumapotoza njira yake,+ choncho mtima wake umakwiyira Yehova.+

  • Yesaya 55:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 “Maganizo a anthu inu si maganizo anga,+ ndipo njira zanga si njira zanu,”+ akutero Yehova.

  • Yesaya 55:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 “Pakuti monga momwe kumwamba kulili pamwamba kuposa dziko lapansi,+ momwemonso njira zanga n’zapamwamba kuposa njira zanu,+ ndiponso maganizo anga ndi apamwamba kuposa maganizo anu.+

  • Ezekieli 18:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 “‘Anthu inu mudzanena kuti: “Njira za Yehova n’zopanda chilungamo.”+ Tamverani inu a nyumba ya Isiraeli. Kodi njira zanga ndiye zopanda chilungamo?+ Kodi njira za anthu inu sindizo zopanda chilungamo?+

  • Ezekieli 18:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 “‘Ndithu nyumba ya Isiraeli idzanena kuti: “Njira za Yehova n’zopanda chilungamo.”+ Kodi njira zanga ndiye zopanda chilungamo, inu a nyumba ya Isiraeli?+ Kodi njira za anthu inu sindizo zopanda chilungamo?’+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena