Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yobu 34:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  5 Pakuti Yobu wanena kuti, ‘Ndithu ine si ine wolakwa,+

      Koma Mulungu wapotoza chiweruzo changa.+

  • Yobu 35:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  2 “Kodi mukuona ngati chimenechi n’chilungamo?

      Inuyo mwanena kuti, ‘Ndine wolungama kuposa Mulungu.’+

  • Miyambo 19:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Kupusa kwa munthu wochokera kufumbi n’kumene kumapotoza njira yake,+ choncho mtima wake umakwiyira Yehova.+

  • Ezekieli 33:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 “Anthu a mtundu wako anena kuti, ‘Njira za Yehova n’zopanda chilungamo,’+ komatu njira zawo ndiye zopanda chilungamo.

  • Malaki 2:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 “Anthu inu mwatopetsa Yehova ndi mawu anu,+ ndipo mwanena kuti, ‘Tamutopetsa motani?’ Mwa kunena kuti, ‘Aliyense wochita zoipa ndi wabwino kwa Yehova, ndipo iye amakondwera ndi anthu otero.’+ Kapena mwa kunena kuti, ‘Kodi Mulungu wachilungamo ali kuti?’”+

  • Aroma 9:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Munthu iwe!+ Iweyo ndiwe ndani kuti uziyankhana ndi Mulungu?+ Kodi chinthu choumbidwa chinganene kwa munthu amene anachiumba kuti, “Unandipangiranji motere?”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena