Levitiko 26:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Ine ndidzakubalalitsani pakati pa anthu a mitundu ina,+ ndipo ndidzakusololerani lupanga ndi kukupitikitsani.+ Dziko lanu lidzakhala bwinja,+ ndipo mizinda yanu idzawonongedwa ndi kukhala mabwinja. Yeremiya 42:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 ndiye kuti lupanga limene mukuliopa lidzakupezani ku Iguputo+ komweko ndipo njala yaikulu imene mukuithawa idzakutsatirani ku Iguputoko+ moti mudzafera komweko.+ Ezekieli 12:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Anthu onse omuzungulira amene amamuthandiza, ndiponso magulu ake onse ankhondo, ndidzawabalalitsira ku mphepo zonse zinayi,+ ndipo ndidzawatsatira nditasolola lupanga.+
33 Ine ndidzakubalalitsani pakati pa anthu a mitundu ina,+ ndipo ndidzakusololerani lupanga ndi kukupitikitsani.+ Dziko lanu lidzakhala bwinja,+ ndipo mizinda yanu idzawonongedwa ndi kukhala mabwinja.
16 ndiye kuti lupanga limene mukuliopa lidzakupezani ku Iguputo+ komweko ndipo njala yaikulu imene mukuithawa idzakutsatirani ku Iguputoko+ moti mudzafera komweko.+
14 Anthu onse omuzungulira amene amamuthandiza, ndiponso magulu ake onse ankhondo, ndidzawabalalitsira ku mphepo zonse zinayi,+ ndipo ndidzawatsatira nditasolola lupanga.+