Ezekieli 43:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Kumeneko ndinaona ulemerero+ wa Mulungu wa Isiraeli ukubwera kuchokera kumbali ya kum’mawa.+ Mawu ake anali kumveka ngati mkokomo wa madzi ambiri,+ ndipo dziko lapansi linawala chifukwa cha ulemerero wake.+ Chivumbulutso 1:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Mapazi ake anali ngati mkuwa woyengedwa+ bwino ukamanyezimira m’ng’anjo, ndipo mawu+ ake anali ngati mkokomo wa madzi ambiri. Chivumbulutso 14:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Kenako ndinamva phokoso kumwamba ngati mkokomo wa madzi ambiri,+ ndiponso ngati phokoso la bingu lamphamvu. Phokoso ndinamvalo linali ngati la oimba amene akuimba motsagana ndi azeze awo.+
2 Kumeneko ndinaona ulemerero+ wa Mulungu wa Isiraeli ukubwera kuchokera kumbali ya kum’mawa.+ Mawu ake anali kumveka ngati mkokomo wa madzi ambiri,+ ndipo dziko lapansi linawala chifukwa cha ulemerero wake.+
15 Mapazi ake anali ngati mkuwa woyengedwa+ bwino ukamanyezimira m’ng’anjo, ndipo mawu+ ake anali ngati mkokomo wa madzi ambiri.
2 Kenako ndinamva phokoso kumwamba ngati mkokomo wa madzi ambiri,+ ndiponso ngati phokoso la bingu lamphamvu. Phokoso ndinamvalo linali ngati la oimba amene akuimba motsagana ndi azeze awo.+