Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yoswa 11:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Yehova analola mitunduyo kuumitsa mitima+ yawo kuti ichite nkhondo ndi Aisiraeli. Anatero kuti iye awawononge ndi kuti Aisiraeliwo asawamvere chisoni,+ koma kuti awatheretu monga mmene Yehova analamulira Mose.+

  • Salimo 95:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  8 Musaumitse mitima yanu monga mmene makolo anu anachitira pa Meriba,+

      Monga mmene anachitira pa Masa m’chipululu,+

  • Ezekieli 3:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Koma a nyumba ya Isiraeli sakafuna kukumvera, chifukwa iwo safuna kundimvera.+ Pakuti anthu onse a nyumba ya Isiraeli ndi amakani ndi osamva.+

  • Aheberi 3:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Tichite zimenezi pamene Malemba akunena kuti: “Lero anthu inu mukamvera mawu a Mulungu,+ musaumitse mitima yanu ngati mmene zinakhalira pamene makolo anu anandipsetsa mtima.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena