-
Danieli 8:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Ndiyeno ndinamva woyera winawake+ akulankhula ndipo woyera wina anafunsa woyera amene anali kulankhulayo kuti: “Kodi masomphenya okhudza nsembe yoyenera kuperekedwa nthawi zonse,+ tchimo lobweretsa chiwonongeko+ ndiponso kupondedwapondedwa kwa malo opatulika ndi kwa khamulo,+ adzakhala a nthawi yaitali bwanji?”
-