Ezekieli 23:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 “Ohola anayamba kuchita uhule+ ngakhale kuti anali mkazi wanga. Anali kulakalaka kwambiri amuna amene ankakhumba kugona naye.+ Anali kulakalaka Asuri+ amene anali kukhala moyandikana naye. Hoseya 4:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Anthu anga amafunsira zinthu kwa mafano+ awo amtengo+ ndipo ndodo za m’manja mwawo zimawauza zochita. Amachita zimenezi chifukwa chakuti mtima wadama wawasocheretsa+ ndipo asiya kugonjera Mulungu wawo chifukwa cha damalo.+
5 “Ohola anayamba kuchita uhule+ ngakhale kuti anali mkazi wanga. Anali kulakalaka kwambiri amuna amene ankakhumba kugona naye.+ Anali kulakalaka Asuri+ amene anali kukhala moyandikana naye.
12 Anthu anga amafunsira zinthu kwa mafano+ awo amtengo+ ndipo ndodo za m’manja mwawo zimawauza zochita. Amachita zimenezi chifukwa chakuti mtima wadama wawasocheretsa+ ndipo asiya kugonjera Mulungu wawo chifukwa cha damalo.+