Salimo 85:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Kukoma mtima kosatha ndi choonadi zakumana.+Chilungamo ndi mtendere zapsompsonana.+ Yeremiya 4:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndipo ngati udzalumbira+ kuti, ‘Pali Yehova Mulungu wamoyo, Mulungu wachoonadi+ ndi chilungamo,’+ pamenepo mitundu ya anthu idzapeza madalitso* kudzera mwa iye ndipo idzadzitama m’dzina lake.”+ Mika 7:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Kodi pali Mulungu winanso wofanana ndi inu+ amene amakhululukira zolakwa+ ndi machimo a anthu ake otsala omwe ndi cholowa chake?+ Inu simudzakhalabe wokwiya mpaka kalekale, pakuti kusonyeza kukoma mtima kosatha kumakusangalatsani.+
2 Ndipo ngati udzalumbira+ kuti, ‘Pali Yehova Mulungu wamoyo, Mulungu wachoonadi+ ndi chilungamo,’+ pamenepo mitundu ya anthu idzapeza madalitso* kudzera mwa iye ndipo idzadzitama m’dzina lake.”+
18 Kodi pali Mulungu winanso wofanana ndi inu+ amene amakhululukira zolakwa+ ndi machimo a anthu ake otsala omwe ndi cholowa chake?+ Inu simudzakhalabe wokwiya mpaka kalekale, pakuti kusonyeza kukoma mtima kosatha kumakusangalatsani.+