Yesaya 8:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Taonani, ine ndi ana amene Yehova wandipatsa+ tili ngati zizindikiro+ ndiponso ngati zozizwitsa mu Isiraeli, zochokera kwa Yehova wa makamu amene amakhala m’phiri la Ziyoni.+ Yesaya 20:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kenako Yehova anati: “Monga momwe mtumiki wanga Yesaya wayendera wopanda zovala ndiponso wopanda nsapato kwa zaka zitatu, kuti akhale chizindikiro+ ndi chenjezo kwa Iguputo+ ndi Itiyopiya,+ Ezekieli 12:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 “Uwauze kuti iweyo ndiwe chizindikiro cholosera zam’tsogolo+ kwa iwo. Zidzachitika kwa iwo monga mmene iwe wachitira. Iwo adzapita ku ukapolo, kudziko lina.+ Ezekieli 24:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ezekieli wakhala chizindikiro cholosera zam’tsogolo.+ Mudzachita zonse zimene iye wachita. Mudzachita zimenezo tsoka lanu likadzafika,+ ndipo mudzadziwa kuti ine ndine Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.’”’”+
18 Taonani, ine ndi ana amene Yehova wandipatsa+ tili ngati zizindikiro+ ndiponso ngati zozizwitsa mu Isiraeli, zochokera kwa Yehova wa makamu amene amakhala m’phiri la Ziyoni.+
3 Kenako Yehova anati: “Monga momwe mtumiki wanga Yesaya wayendera wopanda zovala ndiponso wopanda nsapato kwa zaka zitatu, kuti akhale chizindikiro+ ndi chenjezo kwa Iguputo+ ndi Itiyopiya,+
11 “Uwauze kuti iweyo ndiwe chizindikiro cholosera zam’tsogolo+ kwa iwo. Zidzachitika kwa iwo monga mmene iwe wachitira. Iwo adzapita ku ukapolo, kudziko lina.+
24 Ezekieli wakhala chizindikiro cholosera zam’tsogolo.+ Mudzachita zonse zimene iye wachita. Mudzachita zimenezo tsoka lanu likadzafika,+ ndipo mudzadziwa kuti ine ndine Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.’”’”+