Salimo 112:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Woipa adzaona zimenezi ndipo adzasautsika.+ ש [Shin]Adzakukuta mano ndi kusungunuka.+ ת [Taw]Chikhumbo cha anthu oipa chidzatha.+ Mateyu 8:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 pamene ana a ufumuwo+ adzaponyedwa kunja kumdima. Kumeneko adzalira ndi kukukuta mano.”+ Mateyu 13:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Kenako adzawaponya m’ng’anjo yamoto.+ Kumeneko adzalira ndi kukukuta mano.+ Mateyu 24:51 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 51 Pamenepo adzam’patsa chilango choopsa+ ndipo adzam’ponya kumene kuli anthu onyenga. Kumeneko ndiye kudzakhala kulira ndi kukukuta mano.+ Mateyu 25:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Ponyani kapolo wopanda pake ameneyu kunja kumdima. Kumeneko kudzakhala kulira ndi kukukuta mano.’+
10 Woipa adzaona zimenezi ndipo adzasautsika.+ ש [Shin]Adzakukuta mano ndi kusungunuka.+ ת [Taw]Chikhumbo cha anthu oipa chidzatha.+
51 Pamenepo adzam’patsa chilango choopsa+ ndipo adzam’ponya kumene kuli anthu onyenga. Kumeneko ndiye kudzakhala kulira ndi kukukuta mano.+
30 Ponyani kapolo wopanda pake ameneyu kunja kumdima. Kumeneko kudzakhala kulira ndi kukukuta mano.’+