Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 6:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Ukachititse anthu awa kuumitsa mtima wawo,+ ndipo ukachititse makutu awo kuti asamamve.+ Ukamate maso awo kuti asamaone ndi maso awowo, ndiponso kuti asamamve ndi makutu awo, komanso kuti mtima wawo usamvetsetse zinthu, kuti angatembenuke n’kuchira.”+

  • Yeremiya 5:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 “Tsopano tamverani izi anthu opusa inu, anthu opanda nzeru mumtima mwanu,+ amene muli ndi maso koma simukuona,+ muli ndi makutu koma simukumva.+

  • Ezekieli 12:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 “Iwe mwana wa munthu, ukukhala pakati pa anthu opanduka+ omwe ali ndi maso koma saona,+ omwe ali ndi makutu koma samva,+ chifukwa ndi anthu opanduka.+

  • Maliko 4:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 kuti kupenya azipenya ndithu, koma osaona, ndi kuti kumva azimva ndithu, koma osazindikira tanthauzo lake, kutinso asatembenuke ndi kukhululukidwa.”+

  • Maliko 8:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 ‘Ngakhale kuti muli maso, kodi simuona? Ndipo ngakhale kuti muli ndi makutu kodi simumva?’+ Komanso simukukumbukira kodi,

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena