Mateyu 16:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Poyankha, Simoni Petulo ananena kuti: “Ndinu Khristu,+ Mwana wa Mulungu wamoyo.”+ Luka 4:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Ziwanda nazonso zinatuluka mwa anthu ambiri.+ Zinali kufuula kuti: “Inu ndinu Mwana+ wa Mulungu.” Koma iye anali kudzudzula ziwandazo, ndipo sanali kuzilola kuti zilankhule,+ chifukwa zinali kudziwa kuti iye+ ndi Khristu.+ Yohane 1:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Choyamba iyeyu anapeza m’bale wake Simoni, ndi kumuuza kuti: “Ifetu tapeza Mesiya”+ (dzina lotanthauza, Khristu,+ polimasulira). Yohane 6:69 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 69 Ife takhulupirira ndipo tadziwa kuti inu ndinu Woyera wa Mulungu.”+
41 Ziwanda nazonso zinatuluka mwa anthu ambiri.+ Zinali kufuula kuti: “Inu ndinu Mwana+ wa Mulungu.” Koma iye anali kudzudzula ziwandazo, ndipo sanali kuzilola kuti zilankhule,+ chifukwa zinali kudziwa kuti iye+ ndi Khristu.+
41 Choyamba iyeyu anapeza m’bale wake Simoni, ndi kumuuza kuti: “Ifetu tapeza Mesiya”+ (dzina lotanthauza, Khristu,+ polimasulira).