Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Mateyu 16:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Pakuti aliyense wofuna kupulumutsa moyo wake adzautaya, koma aliyense wotaya moyo wake chifukwa cha ine adzaupeza.+

  • Maliko 8:35
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 35 Pakuti aliyense wofuna kupulumutsa moyo wake adzautaya. Koma aliyense wotaya moyo wake chifukwa cha ine ndi uthenga wabwino, adzaupulumutsa.+

  • Yohane 12:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Aliyense wokonda moyo wake akuuwononga, koma wodana ndi moyo wake+ m’dziko lino akuusungira moyo wosatha.+

  • Machitidwe 20:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Komabe, moyo wanga sindikuuona ngati wofunika kapena wamtengo wapatali kwa ine ayi.+ Chimene ndikungofuna n’chakuti ndimalize kuthamanga mpikisano umenewu,+ komanso kuti ndimalize utumiki+ umene ndinalandira+ kwa Ambuye Yesu basi. Ndikungofuna kuchitira umboni mokwanira za uthenga wabwino wa kukoma mtima kwakukulu kwa Mulungu.+

  • Chivumbulutso 2:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Usachite mantha ndi mavuto amene ukumane nawo.+ Taona! Mdyerekezi+ adzapitiriza kuponya m’ndende ena a inu, kuti muyesedwe mpaka pamapeto,+ ndipo mudzakhala m’masautso+ masiku 10. Sonyeza kukhulupirika kwako mpaka imfa,+ ndipo ndidzakupatsa mphoto* ya moyo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena