Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Mateyu 24:44
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 44 Pa chifukwa chimenechi, nanunso khalani okonzeka,+ chifukwa pa ola limene simukuliganizira, Mwana wa munthu adzabwera.

  • Mateyu 25:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 “Chotero khalanibe maso+ chifukwa simukudziwa tsiku kapena ola lake.+

  • Maliko 13:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Ndipo anthu onse adzadana nanu chifukwa cha dzina langa.+ Koma amene adzapirire mpaka pa mapeto,+ ndiye amene adzapulumuke.+

  • 2 Petulo 3:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Muzichita zimenezi poyembekezera+ ndi kukumbukira nthawi zonse kukhalapo kwa tsiku la Yehova,+ pamene kumwamba kudzapsa ndi moto n’kusungunuka,+ ndipo zinthu zimene zimapanga kumwamba ndi dziko lapansi zidzatentha kwambiri n’kusungunuka.

  • Chivumbulutso 3:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Choncho, pitiriza kukumbukira zimene unalandira+ ndi zimene unamva. Pitiriza kuzitsatira,+ ndipo ulape.+ Ndithudi, ukapanda kudzuka,+ ndidzabwera ngati mbala,+ ndipo sudzadziwa ngakhale pang’ono ola limene ndidzafike kwa iwe.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena