Salimo 80:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Munachititsa mtengo wa mpesa kuchoka mu Iguputo.+Munapitikitsa mitundu ya anthu kuti mubzalemo mtengowo.+ Yeremiya 2:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Koma ine ndinakubzala ngati mtengo wa mpesa wofiira, wabwino kwambiri.+ Mtengo wonsewo unali mbewu yeniyeni yabwino. Ndiye wandisinthira bwanji kukhala mphukira yachabechabe ya mtengo wa mpesa wachilendo?’+ 1 Akorinto 3:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pakuti ndife antchito anzake a Mulungu.+ Inuyo ndinu munda wa Mulungu umene ukulimidwa,+ nyumba ya Mulungu.+
8 Munachititsa mtengo wa mpesa kuchoka mu Iguputo.+Munapitikitsa mitundu ya anthu kuti mubzalemo mtengowo.+
21 Koma ine ndinakubzala ngati mtengo wa mpesa wofiira, wabwino kwambiri.+ Mtengo wonsewo unali mbewu yeniyeni yabwino. Ndiye wandisinthira bwanji kukhala mphukira yachabechabe ya mtengo wa mpesa wachilendo?’+
9 Pakuti ndife antchito anzake a Mulungu.+ Inuyo ndinu munda wa Mulungu umene ukulimidwa,+ nyumba ya Mulungu.+