Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Aroma 8:30
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 30 Ndiponso, amene anawasankhiratu+ ndi amenenso anawaitana,+ ndipo amene anawaitanawo ndi amenenso anawayesa olungama.+ Kenako amene anawayesa olungama ndi amenenso anawapatsa ulemerero.+

  • 1 Akorinto 13:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Pakuti pa nthawi ino sitikuona bwinobwino chifukwa tikugwiritsa ntchito galasi losaoneka bwinobwino,+ koma pa nthawiyo zidzakhala maso ndi maso.+ Pa nthawi ino zimene ndikudziwa n’zoperewera, koma pa nthawiyo ndidzadziwa bwinobwino ngati mmene ineyo ndikudziwikira bwinobwino.+

  • 1 Petulo 1:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Anatibereka kuti tikhale ndi cholowa chosawonongeka,+ chosadetsedwa ndiponso chosasuluka. Cholowa chimenechi anasungira inuyo kumwamba,+

  • 1 Yohane 3:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Okondedwa, tsopano ndife ana a Mulungu,+ koma padakali pano sizinaonekerebe kuti tidzakhala otani.+ Tikudziwa kuti akadzaonekera,+ tidzakhala ngati iyeyo,+ chifukwa tidzamuona mmene alili.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena