Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Aroma 3:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Choncho palibe munthu amene amaonedwa wolungama ndi Mulungu chifukwa chotsatira Chilamulo,+ popeza Chilamulo chimatithandiza kudziwa bwino uchimo.+

  • Aheberi 7:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Chilamulo sichinapangitse chilichonse kukhala changwiro.+ Koma chiyembekezo cha zinthu zabwino chimene anabweretsa,+ chomwe chikutithandiza kuyandikira Mulungu,+ chinachita zimenezi.

  • Aheberi 9:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Chihema chimenecho chinali chifaniziro cha nthawi inoyo+ ndipo mogwirizana ndi chifanizirocho, mphatso ndiponso nsembe zimaperekedwa.+ Komabe, zimenezi sizipangitsa munthu amene akuchita utumiki wopatulikayo kukhala ndi chikumbumtima choyera.+

  • Aheberi 10:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Popeza Chilamulo chimangochitira chithunzi+ zinthu zabwino zimene zikubwera+ ndipo si zinthu zenizenizo, sichingachititse* amene amalambira Mulungu kukhala angwiro pogwiritsa ntchito nsembe zimene amapereka mosalekeza chaka chilichonse.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena