Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Chivumbulutso 5
  • Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

Zimene Zili Mʼbuku la Chivumbulutso

      • Mpukutu umene anaumata ndi zidindo 7 (1-5)

      • Mwanawankhosa anatenga mpukutuwo (6-8)

      • Mwanawankhosa ndi woyenera kumatula zidindozo (9-14)

Chivumbulutso 5:1

Mawu a M'munsi

  • *

    Mʼchilankhulo choyambirira, “mkati ndi kunja komwe.”

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 4:2, 3

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 82-83

Chivumbulutso 5:2

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 82-83

Chivumbulutso 5:3

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 82-83

Chivumbulutso 5:4

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 82-83

Chivumbulutso 5:5

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Ge 49:9, 10; Ahe 7:14
  • +Yes 11:1, 10; Aro 15:12
  • +2Sa 7:8, 12; Chv 22:16
  • +Yoh 16:33

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    “Wotsatira Wanga,” ptsa. 35-36

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 83-84

    Nsanja ya Olonda,

    8/15/1994, tsa. 31

Chivumbulutso 5:6

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Yes 53:7; Yoh 1:29; 1Pe 1:19
  • +Yoh 19:30; Chv 5:12
  • +Aef 1:22
  • +Chv 1:4

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    1/15/2009, tsa. 30

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 55, 84-85

Chivumbulutso 5:7

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Sl 47:8; Yes 6:1

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 85

Chivumbulutso 5:8

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 5:14; 19:4
  • +Sl 141:2; Chv 8:4

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 85-87

Chivumbulutso 5:9

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Sl 33:3; 144:9; Yes 42:10; Chv 14:3
  • +Mt 26:27, 28; 1Ak 6:20; Ahe 9:12; 1Pe 1:18, 19
  • +Chv 14:4

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 31

    Nsanja ya Olonda (Yogawira),

    No. 6 2016, tsatsa. 6-7

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 85-88

    Mtendere Weniweni, ptsa. 65-66

Chivumbulutso 5:10

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Lu 12:32; 22:28-30
  • +Eks 19:6; 1Pe 2:9; Chv 1:5, 6
  • +Mt 19:28; Chv 20:4, 6; 22:5

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 31

    Nsanja ya Olonda (Yogawira),

    No. 6 2016, tsatsa. 6-7

    Nsanja ya Olonda,

    8/15/2006, ptsa. 6-7

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 87-88

Chivumbulutso 5:11

Mawu a M'munsi

  • *

    Mʼchilankhulo choyambirira, “miyanda kuchulukitsa ndi miyanda.”

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Da 7:9, 10

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 24

    Galamukani!,

    4/2011, tsa. 29

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 88

    Nsanja ya Olonda,

    5/15/1987, tsa. 12

Chivumbulutso 5:12

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Yes 53:7; Chv 5:6
  • +Mt 28:18

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 88

Chivumbulutso 5:13

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Afi 2:9, 10
  • +Chv 4:2, 3
  • +Yoh 1:29; Chv 7:17
  • +Yoh 5:23; 1Ti 6:16
  • +1Pe 4:11

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    3/2017, ptsa. 8-9

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 88-89

Chivumbulutso 5:14

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 89

Mabaibulo Ena

Dinani pa nambala ya vesi kuti muone mavesi a m'Baibulo lina ofanana ndi vesilo.

Malemba Ena

Chiv. 5:1Chv 4:2, 3
Chiv. 5:5Ge 49:9, 10; Ahe 7:14
Chiv. 5:5Yes 11:1, 10; Aro 15:12
Chiv. 5:52Sa 7:8, 12; Chv 22:16
Chiv. 5:5Yoh 16:33
Chiv. 5:6Yes 53:7; Yoh 1:29; 1Pe 1:19
Chiv. 5:6Yoh 19:30; Chv 5:12
Chiv. 5:6Aef 1:22
Chiv. 5:6Chv 1:4
Chiv. 5:7Sl 47:8; Yes 6:1
Chiv. 5:8Chv 5:14; 19:4
Chiv. 5:8Sl 141:2; Chv 8:4
Chiv. 5:9Sl 33:3; 144:9; Yes 42:10; Chv 14:3
Chiv. 5:9Mt 26:27, 28; 1Ak 6:20; Ahe 9:12; 1Pe 1:18, 19
Chiv. 5:9Chv 14:4
Chiv. 5:10Lu 12:32; 22:28-30
Chiv. 5:10Eks 19:6; 1Pe 2:9; Chv 1:5, 6
Chiv. 5:10Mt 19:28; Chv 20:4, 6; 22:5
Chiv. 5:11Da 7:9, 10
Chiv. 5:12Yes 53:7; Chv 5:6
Chiv. 5:12Mt 28:18
Chiv. 5:13Afi 2:9, 10
Chiv. 5:13Chv 4:2, 3
Chiv. 5:13Yoh 1:29; Chv 7:17
Chiv. 5:13Yoh 5:23; 1Ti 6:16
Chiv. 5:131Pe 4:11
  • Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
  • Werengani mu Baibulo la Dziko Latsopano
  • 1
  • 2
  • 3
  • 4
  • 5
  • 6
  • 7
  • 8
  • 9
  • 10
  • 11
  • 12
  • 13
  • 14
Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
Chivumbulutso 5:1-14

Chivumbulutso Chimene Yohane Analandira

5 Kenako ndinaona mpukutu umene unalembedwa mbali zonse,* uli mʼdzanja lamanja la Mulungu amene anakhala pampando wachifumu.+ Mpukutuwo anaumata molimba ndi zidindo 7 zomatira. 2 Ndipo ndinaona mngelo wamphamvu akulengeza ndi mawu okweza kuti: “Ndi ndani ali woyenera kumatula zidindo zimene amatira mpukutuwu nʼkuutsegula?” 3 Koma panalibe aliyense kaya kumwamba, padziko lapansi kapena pansi pa nthaka, amene anatha kutsegula mpukutuwo kapena kuyangʼanamo ndi kuuwerenga. 4 Choncho ndinalira kwambiri chifukwa sipanapezeke wina aliyense woyenera kutsegula mpukutuwo kapena kuyangʼanamo nʼkuuwerenga. 5 Koma mmodzi wa akulu aja anandiuza kuti: “Tonthola. Taona! Mkango wa fuko la Yuda,+ muzu+ wa Davide,+ anapambana pankhondo+ moti ndi woyenera kumatula zidindo 7 zimene amatira mpukutuwo nʼkuutsegula.”

6 Kenako ndinaona mwana wa nkhosa+ amene ankaoneka ngati waphedwa,+ ataimirira pakati pa mpando wachifumu ndi angelo 4 aja komanso pakati pa akulu aja.+ Iye anali ndi nyanga 7 ndiponso maso 7. Maso amenewa akuimira mizimu 7 ya Mulungu,+ imene yatumizidwa padziko lonse lapansi. 7 Nthawi yomweyo iye anapita nʼkukatenga mpukutu umene unali mʼdzanja lamanja la Mulungu amene anakhala pampando wachifumu.+ 8 Atatenga mpukutuwo, angelo 4 ndi akulu 24 aja+ anagwada nʼkuwerama pamaso pa Mwanawankhosa. Aliyense wa iwo anali ndi zeze komanso mbale yagolide yodzaza ndi zofukiza. (Zofukizazo zikuimira mapemphero a oyera.)+ 9 Iwo ankaimba nyimbo yatsopano+ yakuti: “Inu ndinu woyenera kutenga mpukutuwo ndi kumatula zidindo zake zomatira, chifukwa munaphedwa ndipo ndi magazi anu munagula anthu kuti atumikire Mulungu.+ Anthuwo ndi ochokera mu fuko lililonse, chilankhulo chilichonse, mtundu uliwonse ndi dziko lililonse.+ 10 Ndipo munawapanga kuti akhale mafumu+ ndi ansembe a Mulungu wathu,+ moti adzakhala mafumu+ olamulira dziko lapansi.”

11 Kenako, ndinaona ndi kumva mawu a angelo ambiri atazungulira mpando wachifumu limodzi ndi angelo 4 komanso akulu aja. Chiwerengero chawo chinali 10 sauzande kuchulukitsa ndi 10 sauzande* ndiponso mamiliyoni kuchulukitsa ndi masauzande.+ 12 Iwo ankanena mofuula kuti: “Mwanawankhosa amene anaphedwa+ ndi woyenera kulandira mphamvu, chuma, nzeru, nyonga, ulemu, ulemerero ndi madalitso.”+

13 Ndipo cholengedwa chilichonse chakumwamba, padziko lapansi, pansi pa nthaka,+ panyanja, ndi zinthu zonse zammenemo, ndinazimva zikunena kuti: “Mulungu amene wakhala pampando wachifumu+ komanso Mwanawankhosa,+ atamandidwe, alandire ulemu,+ ulemerero komanso mphamvu mpaka kalekale.”+ 14 Ndiyeno angelo 4 aja ankanena kuti: “Ame!” Ndipo akulu aja ankagwada nʼkuwerama ndi kulambira Mulungu.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena