Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Chivumbulutso 7
  • Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

Zimene Zili Mʼbuku la Chivumbulutso

      • Angelo 4 anagwira mphepo kuti zisawononge (1-3)

      • Anthu okwana 144,000 anaikidwa chidindo (4-8)

      • Khamu lalikulu limene lavala mikanjo yoyera (9-17)

Chivumbulutso 7:1

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    11/15/2013, tsa. 13

    12/15/2007, tsa. 16

    1/1/1993, tsa. 6

    12/15/1987, tsa. 7

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 113-115

Chivumbulutso 7:2

Mawu a M'munsi

  • *

    Kapena kuti, “kuchokera kumʼmawa.”

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 115

Chivumbulutso 7:3

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +2Ak 1:22; Aef 1:13; 4:30
  • +Chv 9:4

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    1/2016, tsa. 23

    Nsanja ya Olonda,

    3/15/2015, tsa. 15

    11/15/2013, tsa. 13

    12/15/2007, tsa. 16

    1/1/2007, ptsa. 30-31

    5/1/1998, tsa. 15

    2/1/1995, ptsa. 9-10

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 115-116, 162, 276-277

Chivumbulutso 7:4

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 14:1, 3
  • +Aro 2:29; 9:6; Aga 6:16; Chv 21:12

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuyankha Mafunso a M’Baibulo,

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 116-119

    Nsanja ya Olonda,

    9/1/2004, ptsa. 30-31

    12/1/1999, tsa. 11

    9/15/1988, ptsa. 6-7

    Kukambitsirana, ptsa. 47, 208

Chivumbulutso 7:5

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 116-119

Chivumbulutso 7:6

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Ge 41:51

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 116-119

Chivumbulutso 7:7

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 116-119

Chivumbulutso 7:8

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 116-119

Chivumbulutso 7:9

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Yes 2:2; Chv 15:4
  • +Chv 7:14
  • +Le 23:40; Yoh 12:13

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    5/2022, tsa. 16

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    1/2021, tsa. 16

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    9/2019, ptsa. 26-31

    Utumiki Komanso Moyo Wathu,

    12/2019, tsa. 2

    Yeremiya, tsa. 176

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 119-124, 127, 202-203

    Lambirani Mulungu, ptsa. 120-127

    Nsanja ya Olonda,

    5/15/2001, ptsa. 14-15

    12/1/1999, ptsa. 11-12, 17

    4/15/1995, tsa. 31

    2/1/1995, ptsa. 13, 14-19

    5/1/1993, ptsa. 17-18

    5/15/1988, tsa. 15

    5/1/1986, tsa. 18

    Boma, tsa. 28

    Galamukani!,

    12/8/1990, ptsa. 9-10

    Kukambitsirana, tsa. 209

    Chisungiko cha Padziko Lonse, ptsa. 68-70, 72, 116-120, 164-166

Chivumbulutso 7:10

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 4:2, 3
  • +Mac 4:12; Chv 5:6

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 122-123

    Nsanja ya Olonda,

    2/1/1995, tsa. 19

    Kukambitsirana, tsa. 209

    Chisungiko cha Padziko Lonse, tsa. 72

Chivumbulutso 7:11

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 4:4; 11:16

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    1/2021, tsa. 16

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 124

Chivumbulutso 7:12

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 4:11

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    1/2021, tsa. 16

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 124

Chivumbulutso 7:13

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 7:9

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    1/15/2009, tsa. 31

    1/1/2007, ptsa. 27-28

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 125

Chivumbulutso 7:14

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mt 24:21; Mko 13:19
  • +Yoh 1:29; Ahe 9:14; 1Yo 1:7; Chv 1:5

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    1/2021, tsa. 16

    Yeremiya, tsa. 176

    Nsanja ya Olonda,

    3/15/2009, ptsa. 18-19

    1/15/2009, tsa. 31

    1/15/2008, tsa. 25

    1/1/2007, ptsa. 27-28

    11/1/2006, tsa. 26

    11/15/2000, tsa. 13

    2/15/1995, ptsa. 11, 13-17

    2/1/1995, ptsa. 15-16, 19

    6/15/1991, ptsa. 14-15

    2/15/1991, tsa. 18

    5/1/1986, tsa. 18

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 125-126

    Lambirani Mulungu, ptsa. 121-125

    Kukambitsirana, tsa. 216

    Chisungiko cha Padziko Lonse, ptsa. 164-166

Chivumbulutso 7:15

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 4:2
  • +Sl 15:1; Chv 21:3

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    10/2023, tsa. 29

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    1/2021, tsa. 16

    Utumiki Komanso Moyo Wathu,

    12/2019, tsa. 2

    Nsanja ya Olonda,

    2/15/2010, tsa. 17

    1/15/2010, ptsa. 21, 23

    9/15/2008, tsa. 28

    5/1/2002, ptsa. 30-31

    11/15/2000, tsa. 14

    7/1/1996, ptsa. 20-21

    2/1/1995, ptsa. 15-16, 18-19

    1/1/1988, tsa. 17

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 124, 126

Chivumbulutso 7:16

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Sl 121:6; Yes 49:10

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    1/2021, ptsa. 16-17

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 126-128

Chivumbulutso 7:17

Mawu a M'munsi

  • *

    Mʼchilankhulo choyambirira, “ali pakati.”

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 5:6
  • +Yoh 10:11
  • +Chv 22:1
  • +Yes 25:8; Chv 21:4

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    9/2022, tsa. 16

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    1/2021, ptsa. 16-17

    Nsanja ya Olonda,

    9/15/2010, tsa. 29

    9/15/2008, tsa. 28

    10/1/1994, tsa. 16

    12/15/1991, tsa. 12

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 126, 127-128, 303

Mabaibulo Ena

Dinani pa nambala ya vesi kuti muone mavesi a m'Baibulo lina ofanana ndi vesilo.

Malemba Ena

Chiv. 7:32Ak 1:22; Aef 1:13; 4:30
Chiv. 7:3Chv 9:4
Chiv. 7:4Chv 14:1, 3
Chiv. 7:4Aro 2:29; 9:6; Aga 6:16; Chv 21:12
Chiv. 7:6Ge 41:51
Chiv. 7:9Yes 2:2; Chv 15:4
Chiv. 7:9Chv 7:14
Chiv. 7:9Le 23:40; Yoh 12:13
Chiv. 7:10Chv 4:2, 3
Chiv. 7:10Mac 4:12; Chv 5:6
Chiv. 7:11Chv 4:4; 11:16
Chiv. 7:12Chv 4:11
Chiv. 7:13Chv 7:9
Chiv. 7:14Mt 24:21; Mko 13:19
Chiv. 7:14Yoh 1:29; Ahe 9:14; 1Yo 1:7; Chv 1:5
Chiv. 7:15Chv 4:2
Chiv. 7:15Sl 15:1; Chv 21:3
Chiv. 7:16Sl 121:6; Yes 49:10
Chiv. 7:17Chv 5:6
Chiv. 7:17Yoh 10:11
Chiv. 7:17Chv 22:1
Chiv. 7:17Yes 25:8; Chv 21:4
  • Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
  • Werengani mu Baibulo la Dziko Latsopano
  • 1
  • 2
  • 3
  • 4
  • 5
  • 6
  • 7
  • 8
  • 9
  • 10
  • 11
  • 12
  • 13
  • 14
  • 15
  • 16
  • 17
Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
Chivumbulutso 7:1-17

Chivumbulutso Chimene Yohane Analandira

7 Zimenezi zitatha, ndinaona angelo 4 ataimirira mʼmakona 4 a dziko lapansi. Iwo anali atagwira mwamphamvu mphepo 4 za dziko lapansi, kuti mphepo iliyonse isawombe padziko lapansi, panyanja kapena pamtengo uliwonse. 2 Ndinaonanso mngelo wina akukwera kuchokera kotulukira dzuwa,* ali ndi chidindo cha Mulungu wamoyo. Iye anafuula mokweza mawu kwa angelo 4, amene anapatsidwa mphamvu zowononga dziko lapansi ndi nyanja aja, 3 kuti: “Musawononge dziko lapansi, kapena nyanja, kapena mitengo, mpaka titadinda chidindo+ pazipumi za akapolo a Mulungu wathu.”+

4 Ndiyeno ndinamva chiwerengero cha amene anadindidwa chidindo. Anthu okwana 144,000,+ ochokera mʼfuko lililonse la ana a Isiraeli, anadindidwa chidindo:+

5 Mu fuko la Yuda, anadindamo anthu 12,000.

Mu fuko la Rubeni, 12,000.

Mu fuko la Gadi, 12,000.

6 Mu fuko la Aseri, 12,000.

Mu fuko la Nafitali, 12,000.

Mu fuko la Manase,+ 12,000.

7 Mu fuko la Simiyoni, 12,000.

Mu fuko la Levi, 12,000.

Mu fuko la Isakara, 12,000.

8 Mu fuko la Zebuloni, 12,000.

Mu fuko la Yosefe, 12,000.

Ndipo mu fuko la Benjamini, anadindamo anthu 12,000.

9 Zimenezi zitatha, nditayangʼana ndinaona khamu lalikulu la anthu, amene palibe munthu aliyense amene anatha kuwawerenga, ochokera mʼdziko lililonse, fuko lililonse, mtundu uliwonse ndi chilankhulo chilichonse.+ Iwo anali ataimirira pamaso pa mpando wachifumu ndi pamaso pa Mwanawankhosa, atavala mikanjo yoyera+ ndiponso atanyamula nthambi za kanjedza mʼmanja mwawo.+ 10 Iwo anapitiriza kufuula ndi mawu okweza akuti: “Chipulumutso chathu chachokera kwa Mulungu wathu, amene wakhala pampando wachifumu,+ ndi kwa Mwanawankhosa.”+

11 Angelo onse anali ataima kuzungulira mpando wachifumu, akulu+ komanso angelo 4 aja. Ndipo onse anagwada nʼkuwerama mpaka nkhope zawo pansi, pamaso pa mpando wachifumuwo ndi kulambira Mulungu. 12 Iwo ankanena kuti: “Ame! Mulungu wathu ndi amene ali ndi nzeru, mphamvu komanso nyonga ndipo ndi amene akuyenera kutamandidwa, kupatsidwa ulemerero ndi ulemu komanso kuyamikiridwa mpaka kalekale.+ Ame.”

13 Ndiyeno mmodzi wa akulu aja anandifunsa kuti: “Kodi amene avala mikanjo yoyerawa+ ndi ndani ndipo achokera kuti?” 14 Nthawi yomweyo, ndinamuyankha kuti: “Mbuyanga, mukudziwa ndinu.” Ndipo iye anandiuza kuti: “Amenewa ndi amene atuluka mʼchisautso chachikulu+ ndipo achapa mikanjo yawo nʼkuiyeretsa mʼmagazi a Mwanawankhosa.+ 15 Nʼchifukwa chake ali pamaso pa mpando wachifumu wa Mulungu. Iwo akumuchitira utumiki wopatulika usana ndi usiku mʼkachisi wake, ndipo Amene wakhala pampando wachifumuyo+ adzawaphimba ndi tenti yake kuti awateteze.+ 16 Iwo sadzamvanso njala kapena ludzu. Dzuwa kapena kutentha kulikonse sikudzawawotcha,+ 17 chifukwa Mwanawankhosa,+ amene ali pambali* pa mpando wachifumu, adzawaweta+ nʼkuwatsogolera ku akasupe a madzi a moyo.+ Ndipo Mulungu adzapukuta misozi yonse mʼmaso mwawo.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena