21 Motero anawapatsa mzinda wothawirako+ munthu amene wapha mnzake,+ wa Sekemu,+ ndi malo ake odyetserako ziweto+ m’dera lamapiri la Efuraimu. Anawapatsanso Gezeri+ ndi malo ake odyetserako ziweto,
24Ndiyeno Yoswa anasonkhanitsa pamodzi mafuko onse a Isiraeli ku Sekemu.+ Iye anaitanitsa akulu a Isiraeli,+ atsogoleri, oweruza, ndi akapitawo, ndipo iwo anaima pamaso pa Mulungu woona.+
9Patapita nthawi, Abimeleki+ mwana wa Yerubaala, anapita ku Sekemu+ kwa abale a mayi ake. Kumeneko anayamba kulankhula nawo ndiponso kulankhula ndi banja lonse la bambo a mayi akewo kuti: