1 Samueli 17:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Anali atavala chisoti chamkuwa kumutu kwake ndi chovala chamamba achitsulo. Mkuwa wa chovala chamamba chimenecho+ unali wolemera masekeli* 5,000. 2 Mbiri 26:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Uziya anapitiriza kukonzera gulu lankhondo lonselo zishango,+ mikondo ing’onoing’ono,+ zisoti,+ zovala za mamba achitsulo,+ mauta,+ ndi miyala yoponya ndi gulaye.*+
5 Anali atavala chisoti chamkuwa kumutu kwake ndi chovala chamamba achitsulo. Mkuwa wa chovala chamamba chimenecho+ unali wolemera masekeli* 5,000.
14 Uziya anapitiriza kukonzera gulu lankhondo lonselo zishango,+ mikondo ing’onoing’ono,+ zisoti,+ zovala za mamba achitsulo,+ mauta,+ ndi miyala yoponya ndi gulaye.*+