Levitiko 26:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Chotero adzavomereza kuti iwo komanso makolo awo anayenda motsutsana nane,+ anandichimwira+ ndi kundichitira mosakhulupirika. Oweruza 10:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pamenepo ana a Isiraeli anayamba kufuulira Yehova kuti awathandize.+ Iwo anati: “Takuchimwirani+ inu Mulungu wathu, chifukwa takusiyani ndipo tikutumikira Abaala.”+ 1 Mafumu 8:47 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 47 ndiyeno iwo n’kuzindikira kulakwa kwawo m’dziko limene anawatengeralo+ n’kulapa,+ ndipo akapempha+ chifundo kwa inu m’dziko la adani awo amene awagwira,+ n’kunena kuti, ‘Tachimwa,+ tachita zolakwa,+ ndiponso tachita zinthu zoipa,’+ Salimo 106:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Tachimwa mofanana ndi makolo athu.+Tachita zinthu zosayenera, tachita zinthu zoipa.+
40 Chotero adzavomereza kuti iwo komanso makolo awo anayenda motsutsana nane,+ anandichimwira+ ndi kundichitira mosakhulupirika.
10 Pamenepo ana a Isiraeli anayamba kufuulira Yehova kuti awathandize.+ Iwo anati: “Takuchimwirani+ inu Mulungu wathu, chifukwa takusiyani ndipo tikutumikira Abaala.”+
47 ndiyeno iwo n’kuzindikira kulakwa kwawo m’dziko limene anawatengeralo+ n’kulapa,+ ndipo akapempha+ chifundo kwa inu m’dziko la adani awo amene awagwira,+ n’kunena kuti, ‘Tachimwa,+ tachita zolakwa,+ ndiponso tachita zinthu zoipa,’+