Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 16:46
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 46 Kenako Mose anauza Aroni kuti: “Tenga chofukizira uikemo moto wochokera paguwa lansembe.+ Uikemo nsembe yofukiza n’kupita kwa khamulo mofulumira kuti ukawaphimbire machimo awo.+ Chita zimenezi chifukwa Yehova wakwiya kwambiri.+ Mliritu wayamba kale!”

  • Deuteronomo 28:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Yehova adzachititsa mliri kukumamatira kufikira atakufafaniza m’dziko limene ukupita kukalitenga kukhala lako.+

  • 1 Mbiri 21:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Pamenepo Yehova anagwetsa mliri+ mu Isiraeli, moti mu Isiraeli munafa anthu 70,000.+

  • 1 Mbiri 27:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Yowabu+ mwana wa Zeruya anayamba kuwerenga anthu koma sanamalize.+ Kenako mkwiyo+ wa Mulungu unagwera Isiraeli chifukwa chowerenga anthuwo, ndipo chiwerengerocho sichinalembedwe pa zochitika za m’masiku a Mfumu Davide.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena