3 Ndinali kuonekera kwa Abulahamu,+ Isaki+ ndi Yakobo+ monga Mulungu Wamphamvuyonse.+ Koma za dzina langa lakuti Yehova,+ ine sindinadzidziwikitse+ kwa iwo.
11 Kenako mnyamatayo anayamba kunyoza ndi kutukwana+ dzina la Mulungu.+ Chotero anabwera naye kwa Mose.+ Dzina la mayi ake linali Selomiti, mwana wa Dibiri, wa fuko la Dani.