Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 20:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 chifukwa Yehova Mulungu wanu akuyenda limodzi nanu kuti akumenyereni nkhondo ndi kukupulumutsani kwa adani anu.’+

  • 1 Samueli 1:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Chaka ndi chaka mwamuna ameneyu anali kutuluka mumzinda wake n’kupita ku Silo,+ kukagwada ndi kuweramira pansi+ pamaso pa Yehova wa makamu ndi kupereka nsembe zake. Kumeneko n’kumene ana awiri a Eli, Hofeni ndi Pinihasi,+ anali kutumikira monga ansembe a Yehova.+

  • 1 Samueli 15:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Yehova wa makamu+ wanena kuti, ‘Ndibwezera+ Aamaleki chifukwa choukira Aisiraeli panjira, pamene Aisiraeliwo anali kutuluka mu Iguputo.+

  • 1 Mafumu 18:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Koma Eliya anati: “Pali Yehova wa makamu,+ Mulungu wamoyo amene ndimam’tumikira, lero ndionekera kwa Ahabu.”

  • 1 Mbiri 17:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Dzina lanu+ likhale lokhulupirika ndi lokwezeka+ mpaka kalekale. Anthu anene kuti, ‘Yehova wa makamu+ Mulungu wa Isiraeli,+ ndiye Mulungu wa Isiraeli,’+ ndipo nyumba ya mtumiki wanu Davide ikhalitse pamaso panu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena