Levitiko 19:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 “‘Usamayendeyende pakati pa anthu amtundu wako n’kumachita miseche.+ Usachite kanthu kalikonse kuti uphetse mnzako.+ Ine ndine Yehova. 2 Samueli 19:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Choncho mtumiki wangayo anandinenera+ ine mtumiki wanu miseche kwa inu mbuyanga mfumu. Koma inu mbuyanga mfumu muli ngati mngelo+ wa Mulungu woona, motero chitani zimene zili zabwino kwa inu. Salimo 15:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Iye sanena miseche ndi lilime lake.+Sachitira mnzake choipa,+Ndipo satonza bwenzi lake lapamtima.+ Miyambo 6:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 mboni yachinyengo yonena mabodza,+ ndi aliyense woyambitsa mikangano pakati pa abale.+ Miyambo 26:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Mawu a munthu wonenera ena zoipa ali ngati zinthu zofunika kuzimeza msangamsanga, zimene zimatsikira mkatikati mwa mimba.+
16 “‘Usamayendeyende pakati pa anthu amtundu wako n’kumachita miseche.+ Usachite kanthu kalikonse kuti uphetse mnzako.+ Ine ndine Yehova.
27 Choncho mtumiki wangayo anandinenera+ ine mtumiki wanu miseche kwa inu mbuyanga mfumu. Koma inu mbuyanga mfumu muli ngati mngelo+ wa Mulungu woona, motero chitani zimene zili zabwino kwa inu.
22 Mawu a munthu wonenera ena zoipa ali ngati zinthu zofunika kuzimeza msangamsanga, zimene zimatsikira mkatikati mwa mimba.+