Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 18:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Pakuti ndasunga njira za Yehova,+

      Sindinachoke kwa Mulungu wanga. Ndikanatero, ndikanachita chinthu choipa.+

  • Salimo 71:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Inu Mulungu, mwandiphunzitsa kuyambira pa unyamata wanga,+

      Ndipo mpaka pano ndikunena za ntchito zanu zodabwitsa.+

  • Miyambo 8:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Kuopa Yehova kumatanthauza kudana ndi zoipa.+ Ndimadana ndi kudzikweza, kunyada,+ njira yoipa ndiponso pakamwa ponena zopotoka.+

  • Mlaliki 7:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Ndi bwino kuti usunge malangizo oyambawo, ndipo usasiye malangizo achiwiriwo.+ Pakuti munthu amene amaopa Mulungu adzamvera malangizo onsewa.+

  • Mlaliki 12:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Kumbukira Mlengi wako Wamkulu+ masiku a unyamata wako,+ asanafike masiku oipa+ komanso zisanafike zaka zimene udzati: “Moyo sukundisangalatsa.”+

  • Yesaya 50:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Ndani pakati panu amene amaopa+ Yehova ndi kumvera mawu a mtumiki wake?+ Ndani amayenda mu mdima wokhawokha+ ndipo alibe kuwala? Iye akhulupirire dzina la Yehova+ ndipo adalire Mulungu wake.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena