1 Mafumu 17:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Eliya+ wa ku Tisibe, wochokera ku Giliyadi+ analankhula ndi Ahabu kuti: “Pali Yehova Mulungu wamoyo, Mulungu wa Isiraeli+ amene ndimam’tumikira,+ sikugwa mame kapena mvula+ zaka zikubwerazi, pokhapokha ine nditalamula.”+ Zekariya 10:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 “Pemphani Yehova kuti akugwetsereni mvula+ pa nthawi ya mvula yomalizira.+ Pemphani Yehova amene anapanga mitambo yamvula+ ndiponso amene amagwetsera anthu mvula yamphamvu.+ Iye amapereka mbewu m’munda mwa munthu aliyense.+
17 Eliya+ wa ku Tisibe, wochokera ku Giliyadi+ analankhula ndi Ahabu kuti: “Pali Yehova Mulungu wamoyo, Mulungu wa Isiraeli+ amene ndimam’tumikira,+ sikugwa mame kapena mvula+ zaka zikubwerazi, pokhapokha ine nditalamula.”+
10 “Pemphani Yehova kuti akugwetsereni mvula+ pa nthawi ya mvula yomalizira.+ Pemphani Yehova amene anapanga mitambo yamvula+ ndiponso amene amagwetsera anthu mvula yamphamvu.+ Iye amapereka mbewu m’munda mwa munthu aliyense.+