Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 24:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Ndiyeno anatenga buku la pangano+ ndi kuwerengera anthuwo kuti amve.+ Zitatero anthuwo anati: “Zonse zimene Yehova wanena tidzachita zomwezo ndipo tidzamumvera.”+

  • Deuteronomo 4:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Pamenepo anakuuzani pangano lake,+ Mawu Khumi,*+ ndipo anakulamulani kuti muzilisunga. Kenako analemba Mawu Khumiwo pamiyala iwiri yosema.+

  • Deuteronomo 9:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Nditakwera m’phiri kukalandira miyala iwiri yosema,+ miyala ya pangano limene Yehova anachita nanu,+ ndinakhala m’phirimo masiku 40, usana ndi usiku,+ (sindinadye mkate kapena kumwa madzi,)

  • 1 Mafumu 8:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Mu Likasalo munalibe chilichonse kupatulapo miyala iwiri yosema+ imene Mose anaikamo+ ku Horebe. Anaiikamo nthawi imene Yehova anachita pangano+ ndi ana a Isiraeli, pamene anali kutuluka m’dziko la Iguputo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena