Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 11:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Kenako Yehova anatsika mumtambo+ n’kulankhula naye.+ Anatengako gawo lina la mzimu+ umene unali pa Mose n’kuuika pa aliyense wa akulu 70 amenewo. Ndipo mzimuwo utangokhala pa iwo, anayamba kuchita zinthu ngati aneneri, koma sanadzachitenso kachiwiri.+

  • Numeri 27:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Um’patseko ulemerero wako,+ kuti khamu lonse la ana a Isiraeli lizimumvera.+

  • 2 Mafumu 2:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Iwo atangowoloka, Eliya anauza Elisa kuti: “Pempha chimene ukufuna kuti ndikuchitire ndisanakuchokere.”+ Elisa anati: “Chonde, magawo awiri+ a mzimu+ wanu abwere kwa ine.”+

  • Yesaya 11:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Mzimu wa Yehova udzakhazikika pa iye,+ mzimu wanzeru,+ womvetsa zinthu,+ wolangiza, wamphamvu,+ wodziwa zinthu+ ndi woopa Yehova.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena