1 Samueli 23:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Tsopano Davide anayamba kukhala m’chipululu, m’malo ovuta kufikako. Iye anapitiriza kukhala m’dera lamapiri m’chipululu cha Zifi,+ ndipo Sauli anali kumufunafuna nthawi zonse,+ koma Mulungu sanam’pereke m’manja mwake.+ 1 Samueli 23:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Ndiyeno Davide anachoka kumeneko ndi kukakhala m’malo ovuta kufikako a ku Eni-gedi.+ 1 Samueli 24:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Zitatero, Davide analumbirira Sauli. Kenako Sauliyo anapita kwawo,+ koma Davide ndi amuna amene anali kuyenda naye anapita kumalo ovuta kufikako.+ 1 Mbiri 11:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Pamenepo n’kuti Davide ali m’malo ovuta kufikako,+ ndiponso n’kuti mudzi wa asilikali a Afilisiti+ uli ku Betelehemu.
14 Tsopano Davide anayamba kukhala m’chipululu, m’malo ovuta kufikako. Iye anapitiriza kukhala m’dera lamapiri m’chipululu cha Zifi,+ ndipo Sauli anali kumufunafuna nthawi zonse,+ koma Mulungu sanam’pereke m’manja mwake.+
22 Zitatero, Davide analumbirira Sauli. Kenako Sauliyo anapita kwawo,+ koma Davide ndi amuna amene anali kuyenda naye anapita kumalo ovuta kufikako.+
16 Pamenepo n’kuti Davide ali m’malo ovuta kufikako,+ ndiponso n’kuti mudzi wa asilikali a Afilisiti+ uli ku Betelehemu.