1 Samueli 23:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndiyeno Davide anayamba kufunsira+ kwa Yehova, kuti: “Kodi ndipite kukamenyana ndi Afilisitiwa?” Yehova anayankha Davide kuti: “Pita, ukamenyane ndi Afilisitiwo ndipo ukapulumutse Keila.” 1 Samueli 30:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndiyeno Davide anayamba kufunsira kwa Yehova,+ kuti: “Kodi ndithamangitse gulu la achifwambali? Kodi ndiwapeza?” Pamenepo anamuyankha+ kuti: “Inde athamangitse chifukwa uwapezadi ndi kulanditsa zinthu zimene afunkha.”+ 2 Samueli 5:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ndiyeno Davide anafunsira+ kwa Yehova kuti: “Kodi ndipite kukamenyana ndi Afilisitiwa? Kodi muwapereka m’manja mwanga?” Pamenepo Yehova anauza Davide kuti: “Pita, ndipereka ndithu Afilisitiwa m’manja mwako.”+ Miyambo 3:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Uzim’kumbukira m’njira zako zonse,+ ndipo iye adzawongola njira zako.+
2 Ndiyeno Davide anayamba kufunsira+ kwa Yehova, kuti: “Kodi ndipite kukamenyana ndi Afilisitiwa?” Yehova anayankha Davide kuti: “Pita, ukamenyane ndi Afilisitiwo ndipo ukapulumutse Keila.”
8 Ndiyeno Davide anayamba kufunsira kwa Yehova,+ kuti: “Kodi ndithamangitse gulu la achifwambali? Kodi ndiwapeza?” Pamenepo anamuyankha+ kuti: “Inde athamangitse chifukwa uwapezadi ndi kulanditsa zinthu zimene afunkha.”+
19 Ndiyeno Davide anafunsira+ kwa Yehova kuti: “Kodi ndipite kukamenyana ndi Afilisitiwa? Kodi muwapereka m’manja mwanga?” Pamenepo Yehova anauza Davide kuti: “Pita, ndipereka ndithu Afilisitiwa m’manja mwako.”+