Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 8:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Muzikumbukira Yehova Mulungu wanu, chifukwa ndiye amakupatsani mphamvu kuti mupeze chuma,+ pofuna kusunga pangano lake limene analumbirira makolo anu, monga mmene wachitira lero.+

  • 1 Mbiri 29:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Chuma+ ndi ulemerero+ zimachokera kwa inu. Inu mumalamulira+ chilichonse. M’dzanja lanu muli mphamvu+ ndi nyonga,+ ndipo dzanja lanu limatha kukweza+ ndiponso kupereka mphamvu kwa onse.+

  • 2 Mbiri 25:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Pamenepo Amaziya+ anafunsa munthu wa Mulungu woonayo kuti: “Nanga bwanji za matalente 100 amene ndapereka kwa asilikali a ku Isiraeli aja?”+ Munthu wa Mulungu woonayo anayankha kuti: “Yehova akhoza kukupatsani zambiri kuposa pamenepa.”+

  • Miyambo 10:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Madalitso a Yehova ndi amene amalemeretsa,+ ndipo sawonjezerapo ululu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena