Maliro 1:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Njira zopita ku Ziyoni zikulira, chifukwa palibe amene akupita kuchikondwerero.+Zipata zake zonse zasiyidwa.+ Ansembe+ ake akuusa moyo.*Anamwali ake agwidwa ndi chisoni,+ ndipo iyeyo akumva kuwawa mumtima. Maliro 2:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Zipata+ zake zamira munthaka. Wawononga mipiringidzo yake ndipo waithyolathyola.Mfumu yake ndi akalonga ake ali pakati pa mitundu ina.+ Malamulo sakutsatiridwa.+Aneneri ake sakuonanso masomphenya ochokera kwa Yehova.+
4 Njira zopita ku Ziyoni zikulira, chifukwa palibe amene akupita kuchikondwerero.+Zipata zake zonse zasiyidwa.+ Ansembe+ ake akuusa moyo.*Anamwali ake agwidwa ndi chisoni,+ ndipo iyeyo akumva kuwawa mumtima.
9 Zipata+ zake zamira munthaka. Wawononga mipiringidzo yake ndipo waithyolathyola.Mfumu yake ndi akalonga ake ali pakati pa mitundu ina.+ Malamulo sakutsatiridwa.+Aneneri ake sakuonanso masomphenya ochokera kwa Yehova.+