Oweruza 5:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mawu a anthu ena otunga madzi anamveka pamalo otungira madzi,+Kumeneko anayamba kusimba ntchito zolungama za Yehova,+Anasimba ntchito zolungama za anthu ake okhala m’midzi ya Isiraeli.Atatero m’pamene anthu a Yehova anapita kumizinda. Salimo 17:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Sonyezani kukoma mtima kosatha mwa kuchita zodabwitsa,+ inu Mpulumutsi wa anthu othawira kwa inu,Amene akuthawa anthu ogalukira dzanja lanu lamanja.+ Salimo 60:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kuti okondedwa anu apulumutsidwe,+Tipulumutseni ndi dzanja lanu lamanja ndi kutiyankha.+ Salimo 98:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Yehova wachititsa chipulumutso chake kudziwika.+Chilungamo chake wachisonyeza ku mitundu ya anthu.+
11 Mawu a anthu ena otunga madzi anamveka pamalo otungira madzi,+Kumeneko anayamba kusimba ntchito zolungama za Yehova,+Anasimba ntchito zolungama za anthu ake okhala m’midzi ya Isiraeli.Atatero m’pamene anthu a Yehova anapita kumizinda.
7 Sonyezani kukoma mtima kosatha mwa kuchita zodabwitsa,+ inu Mpulumutsi wa anthu othawira kwa inu,Amene akuthawa anthu ogalukira dzanja lanu lamanja.+
2 Yehova wachititsa chipulumutso chake kudziwika.+Chilungamo chake wachisonyeza ku mitundu ya anthu.+