Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 15:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  9 Mdaniyo anati, ‘Ndiwathamangira,+ ndi kuwapeza!+

      Ndigawa chuma chawo.+ Pamenepo moyo wanga ukhutira ndi zimene ndawachita!

      Ndisolola lupanga langa! Dzanja langa liwawononga!’+

  • 1 Samueli 2:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  3 Musalankhule modzikweza kwambiri anthu inu,

      Pakamwa panu pasatuluke mawu odzikuza,+

      Pakuti Yehova ndi Mulungu wodziwa zonse.+

      Ndipo zochita za anthu, iye amaziyeza molondola.+

  • Salimo 17:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Mitima yawo siimva chisoni,*+

      Ndipo amalankhula modzikuza ndi pakamwa pawo.+

  • Ezekieli 28:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 “Iwe mwana wa munthu, uza mtsogoleri wa Turo kuti, ‘Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti:

      “‘“Chifukwa chakuti wadzikuza mumtima mwako,+ ndipo ukunena kuti, ‘Ndine mulungu.+ Ndakhala pampando wa mulungu+ pakatikati pa nyanja,’+ ngakhale kuti ndiwe munthu wochokera kufumbi+ osati mulungu,+ ndipo umadziona ngati mulungu . . .

  • 2 Petulo 2:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Pakuti amalankhula mawu odzitukumula opanda pake, ndipo pogwiritsa ntchito zilakolako za thupi+ komanso makhalidwe otayirira, amakopa+ amene akungopulumuka+ kumene kwa anthu ochita zolakwa.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena