Salimo 80:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Munachititsa mtengo wa mpesa kuchoka mu Iguputo.+Munapitikitsa mitundu ya anthu kuti mubzalemo mtengowo.+ Yeremiya 2:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Koma ine ndinakubzala ngati mtengo wa mpesa wofiira, wabwino kwambiri.+ Mtengo wonsewo unali mbewu yeniyeni yabwino. Ndiye wandisinthira bwanji kukhala mphukira yachabechabe ya mtengo wa mpesa wachilendo?’+ Mateyu 21:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 “Mverani fanizo lina: Panali munthu wina yemwe analima munda wa mpesa+ ndi kumanga mpanda kuzungulira mundawo. Komanso anakumba dzenje loponderamo mphesa ndi kumanga nsanja.+ Atatero anausiya m’manja mwa alimi n’kupita kudziko lina.+
8 Munachititsa mtengo wa mpesa kuchoka mu Iguputo.+Munapitikitsa mitundu ya anthu kuti mubzalemo mtengowo.+
21 Koma ine ndinakubzala ngati mtengo wa mpesa wofiira, wabwino kwambiri.+ Mtengo wonsewo unali mbewu yeniyeni yabwino. Ndiye wandisinthira bwanji kukhala mphukira yachabechabe ya mtengo wa mpesa wachilendo?’+
33 “Mverani fanizo lina: Panali munthu wina yemwe analima munda wa mpesa+ ndi kumanga mpanda kuzungulira mundawo. Komanso anakumba dzenje loponderamo mphesa ndi kumanga nsanja.+ Atatero anausiya m’manja mwa alimi n’kupita kudziko lina.+