2 Mafumu 21:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Koma sanamvere,+ ndipo Manase anapitiriza kunyengerera anthu kuti achite zinthu zoipa+ kuposa zimene inkachita mitundu+ yomwe Yehova anaiwononga pamaso pa ana a Isiraeli. Yesaya 65:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 anthu amene akundichitira mwano+ nthawi zonse m’maso muli gwa! Amene amapereka nsembe m’minda,+ amene amafukiza nsembe zautsi+ panjerwa, Aroma 1:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Ndiponso monga mmene iwo sanafunire kumudziwa Mulungu molondola,+ iye anawasiya ndi maganizo awo oipa,+ kuti azichita zinthu zosayenerazo,+ Aheberi 4:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Chotero, tiyeni tichite chilichonse chotheka kuti tilowe mu mpumulo umenewo, kuopera kuti wina angagwe ndi kutengera chitsanzo cha kusamvera cha makolo athuwo.+
9 Koma sanamvere,+ ndipo Manase anapitiriza kunyengerera anthu kuti achite zinthu zoipa+ kuposa zimene inkachita mitundu+ yomwe Yehova anaiwononga pamaso pa ana a Isiraeli.
3 anthu amene akundichitira mwano+ nthawi zonse m’maso muli gwa! Amene amapereka nsembe m’minda,+ amene amafukiza nsembe zautsi+ panjerwa,
28 Ndiponso monga mmene iwo sanafunire kumudziwa Mulungu molondola,+ iye anawasiya ndi maganizo awo oipa,+ kuti azichita zinthu zosayenerazo,+
11 Chotero, tiyeni tichite chilichonse chotheka kuti tilowe mu mpumulo umenewo, kuopera kuti wina angagwe ndi kutengera chitsanzo cha kusamvera cha makolo athuwo.+