13“Pa tsiku limenelo,+ kudzakumbidwa chitsime+ kuti a m’nyumba ya Davide ndi anthu okhala mu Yerusalemu adzayeretsedwe ku machimo+ ndi ku zinthu zawo zonyansa.+
17 chifukwa Mwanawankhosa,+ amene ali pambali pa mpando wachifumu, adzawaweta+ ndi kuwatsogolera ku akasupe a madzi+ a moyo. Ndipo Mulungu adzapukuta misozi yonse m’maso mwawo.”+