Deuteronomo 13:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 “Mneneri+ kapena wolota maloto+ akauka pakati panu n’kukupatsani chizindikiro kapena chodabwitsa cholosera zam’tsogolo,+ Yeremiya 14:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndiyeno Yehova anandiyankha kuti: “Aneneriwo akulosera monama m’dzina langa.+ Ine sindinawatume, kuwalamula, kapena kulankhula nawo.+ Maulosi amene akukuuzaniwo anthu inu, ndiwo masomphenya onama, maula, mawu opanda pake+ ndi chinyengo cha mumtima mwawo.+ Yeremiya 23:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 “Ine sindinatumize aneneriwo, koma okha anathamanga. Ine sindinalankhule nawo, koma okha analosera.+ Yeremiya 27:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 “‘Ine sindinawatume,’ watero Yehova, ‘koma iwo akulosera m’dzina langa monama, ndipo mukawamvera ndidzakubalalitsani.+ Inu pamodzi ndi aneneri amene akulosera kwa inuwo mudzatha.’”+ Yeremiya 29:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 “Anthu onse amene ali ku ukapolo uwatumizire uthenga+ wakuti, ‘Ponena za Semaya wa ku Nehelamu, Yehova wanena kuti: “Pakuti Semaya walosera kwa anthu inu, ngakhale kuti ine sindinamutume, ndipo wayesa kukuchititsani kukhulupirira zinthu zonama,+ Ezekieli 13:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Tsoka kwa aneneri opusa,+ amene akungolosera zamumtima mwawo+ pamene sanaone chilichonse.+ Zekariya 13:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pakadzapezeka munthu aliyense wolosera, bambo ake ndi mayi ake amene anamubereka, adzamuuze kuti, ‘Iwe ufa ndithu, chifukwa walankhula zonama m’dzina la Yehova.’ Ndiyeno bambo ndi mayi akewo adzamulase chifukwa chakuti anali kulosera.+ Luka 6:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 “Muli ndi tsoka, anthu onse akamanena zabwino za inu, pakuti zoterezi n’zimene makolo awo akale anachitira aneneri onyenga.+
13 “Mneneri+ kapena wolota maloto+ akauka pakati panu n’kukupatsani chizindikiro kapena chodabwitsa cholosera zam’tsogolo,+
14 Ndiyeno Yehova anandiyankha kuti: “Aneneriwo akulosera monama m’dzina langa.+ Ine sindinawatume, kuwalamula, kapena kulankhula nawo.+ Maulosi amene akukuuzaniwo anthu inu, ndiwo masomphenya onama, maula, mawu opanda pake+ ndi chinyengo cha mumtima mwawo.+
21 “Ine sindinatumize aneneriwo, koma okha anathamanga. Ine sindinalankhule nawo, koma okha analosera.+
15 “‘Ine sindinawatume,’ watero Yehova, ‘koma iwo akulosera m’dzina langa monama, ndipo mukawamvera ndidzakubalalitsani.+ Inu pamodzi ndi aneneri amene akulosera kwa inuwo mudzatha.’”+
31 “Anthu onse amene ali ku ukapolo uwatumizire uthenga+ wakuti, ‘Ponena za Semaya wa ku Nehelamu, Yehova wanena kuti: “Pakuti Semaya walosera kwa anthu inu, ngakhale kuti ine sindinamutume, ndipo wayesa kukuchititsani kukhulupirira zinthu zonama,+
3 Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Tsoka kwa aneneri opusa,+ amene akungolosera zamumtima mwawo+ pamene sanaone chilichonse.+
3 Pakadzapezeka munthu aliyense wolosera, bambo ake ndi mayi ake amene anamubereka, adzamuuze kuti, ‘Iwe ufa ndithu, chifukwa walankhula zonama m’dzina la Yehova.’ Ndiyeno bambo ndi mayi akewo adzamulase chifukwa chakuti anali kulosera.+
26 “Muli ndi tsoka, anthu onse akamanena zabwino za inu, pakuti zoterezi n’zimene makolo awo akale anachitira aneneri onyenga.+