Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 17:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Popeza waiwala+ Mulungu wa chipulumutso chako,+ ndipo Thanthwe+ la chitetezo chako sunalikumbukire, n’chifukwa chake ukulima minda yokongola n’kumabzalamo mphukira ya mlendo.

  • Ezekieli 23:35
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 35 “Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti, ‘Popeza kuti wandiiwala+ ndi kundiponya kumbuyo,+ udzalangidwa chifukwa cha khalidwe lako lotayirira ndi zochita zako zauhule.’”

  • Hoseya 8:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Isiraeli anaiwala amene anamupanga+ ndipo anayamba kumanga akachisi.+ Yuda nayenso anachulukitsa mizinda yokhala ndi mipanda yolimba kwambiri.+ Koma ine ndidzatumiza moto m’mizinda yake ndipo udzanyeketsa nsanja zokhalamo za mumzinda uliwonse.”+

  • Hoseya 13:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Iwe unakhuta chifukwa chakuti unali ndi zakudya zambiri.+ Unakhuta ndipo mtima wako unayamba kudzitukumula.+ N’chifukwa chake unandiiwala.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena