Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 1:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Dziko lanu lawonongedwa.+ Mizinda yanu yatenthedwa ndi moto,+ ndipo alendo akudya zokolola zochokera munthaka yanu, inu mukuona.+ Chilichonse chawonongeka ngati mmene zimakhalira adani akalanda dziko.+

  • Yesaya 5:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Ndamva Yehova wa makamu akulumbira kuti nyumba zambiri, ngakhale zitakhala zikuluzikulu ndiponso zabwino, zidzakhala chinthu chodabwitsa kwambiri ndipo zidzakhala zopanda wokhalamo.+

  • Yesaya 6:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Pamenepo ndinafunsa kuti: “Mpaka liti, Yehova?”+ Iye anayankha kuti: “Mpaka mizinda yawo itawonongedwa n’kukhala bwinja, yopanda wokhalamo. Mpaka nyumba zawo zitakhala zopanda anthu okhalamo, ndiponso mpaka nthaka itawonongekeratu.+

  • Yeremiya 2:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Mikango yamphamvu imamubangulira.+ Imamutulutsira mawu awo.+ Ndipo yapangitsa dziko lake kukhala chinthu chodabwitsa kwa ena. Mizinda yake aiyatsa moto, choncho simukukhala munthu aliyense.+

  • Yeremiya 9:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Yerusalemu ndidzamusandutsa milu ya miyala+ ndiponso malo obisalamo mimbulu.+ Mizinda ya Yuda ndidzaisandutsa mabwinja, malo opanda wokhalamo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena