Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 21:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Uwu ndi uthenga wokhudza Duma: Ndikumva winawake akundifunsa mofuula kuchokera ku Seiri+ kuti: “Mlonda, kodi usiku watsala wotalika bwanji? Mlonda, kodi usiku watsala wotalika bwanji?”+

  • Yeremiya 25:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Yehova anakutumizirani atumiki ake onse aneneri. Anali kudzuka m’mawa kwambiri ndi kuwatumiza, koma inu simunawamvere+ kapena kutchera khutu lanu kuti mumvetsere.+

  • Ezekieli 3:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 “Iwe mwana wa munthu, ine ndakuika kuti ukhale mlonda wa nyumba ya Isiraeli.+ Umve mawu ochokera pakamwa panga ndipo undichenjezere anthuwo.+

  • Habakuku 2:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Ine ndidzaimabe+ pamalo a mlonda ndiponso pakhoma lachitetezo. Ndidzakhala tcheru+ kuti ndione uthenga umene iye adzalankhula kudzera mwa ine+ ndi zimene ndidzayankha pamene iye akundidzudzula.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena