Deuteronomo 4:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 ndikutenga kumwamba ndi dziko lapansi+ lero monga mboni zokutsutsani, kuti mudzafafanizidwa mwamsanga m’dziko limene mukupita kukalitenga mutawoloka Yorodano. Simudzatalikitsa masiku anu m’dzikomo chifukwa mudzawonongedwa ndithu.+ Maliro 2:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Yehova wameza malo okhala a Yakobo. Sanamvere chisoni malo ake alionse.+Mu ukali wake, iye wagwetsa mipanda yolimba kwambiri+ ya mwana wamkazi wa Yuda.Waipitsa ufumu+ ndi akalonga+ ake ndipo wawagwetsera pansi.+ Ezekieli 9:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Chotero inenso diso langa silimva chisoni+ ndipo sindichita chifundo.+ Ndiwabwezera mogwirizana ndi njira zawo.”+
26 ndikutenga kumwamba ndi dziko lapansi+ lero monga mboni zokutsutsani, kuti mudzafafanizidwa mwamsanga m’dziko limene mukupita kukalitenga mutawoloka Yorodano. Simudzatalikitsa masiku anu m’dzikomo chifukwa mudzawonongedwa ndithu.+
2 Yehova wameza malo okhala a Yakobo. Sanamvere chisoni malo ake alionse.+Mu ukali wake, iye wagwetsa mipanda yolimba kwambiri+ ya mwana wamkazi wa Yuda.Waipitsa ufumu+ ndi akalonga+ ake ndipo wawagwetsera pansi.+
10 Chotero inenso diso langa silimva chisoni+ ndipo sindichita chifundo.+ Ndiwabwezera mogwirizana ndi njira zawo.”+